-
1 Akorinto 14:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Chifukwa ngati mothandizidwa ndi mphatso ya mzimu mukutamanda Mulungu, kodi munthu wamba anganene bwanji kuti “Ame” pa pemphero lanu loyamikira, poti sakudziwa zimene mukunena?
-