1 Akorinto 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho malilime* ndi chizindikiro cha osakhulupirira, osati okhulupirira,+ pomwe kunenera ndi chizindikiro cha okhulupirira, osati osakhulupirira. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
22 Choncho malilime* ndi chizindikiro cha osakhulupirira, osati okhulupirira,+ pomwe kunenera ndi chizindikiro cha okhulupirira, osati osakhulupirira.