-
1 Akorinto 14:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Koma ngati nonse mukunenera, ndiyeno mwalowa munthu wosakhulupirira kapena munthu wamba, iye amadzudzulidwa ndiponso kufufuzidwa mosamala ndi nonsenu.
-