1 Akorinto 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mulungu “anaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Koma pamene akunena kuti ‘waika zinthu zonse pansi pake,’+ nʼzodziwikiratu kuti sakuphatikizapo Mulunguyo, amene anaika zinthu zonsezo pansi pa iye.+
27 Mulungu “anaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Koma pamene akunena kuti ‘waika zinthu zonse pansi pake,’+ nʼzodziwikiratu kuti sakuphatikizapo Mulunguyo, amene anaika zinthu zonsezo pansi pa iye.+