-
1 Akorinto 15:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Zinthu zonse zimene zimakhala ndi mnofu sizikhala zofanana. Anthu, nyama, mbalame ndiponso nsomba zili ndi mnofu, koma chilichonse nʼchosiyana ndi chinzake.
-