1 Akorinto 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Timoteyo+ akadzafika mudzaonetsetse kuti asadzakhale ndi mantha pakati panu, chifukwa iye akugwira ntchito ya Yehova,*+ ngati mmene inenso ndikuchitira. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:10 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, ptsa. 14-15
10 Timoteyo+ akadzafika mudzaonetsetse kuti asadzakhale ndi mantha pakati panu, chifukwa iye akugwira ntchito ya Yehova,*+ ngati mmene inenso ndikuchitira.