1 Akorinto 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abale, mukudziwa kuti anthu a mʼbanja la Sitefana ndi amene anali oyamba kukhala okhulupirira* ku Akaya ndipo anadzipereka kutumikira oyera. Choncho ndikukulimbikitsani kuti, 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:15 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, ptsa. 19-20
15 Abale, mukudziwa kuti anthu a mʼbanja la Sitefana ndi amene anali oyamba kukhala okhulupirira* ku Akaya ndipo anadzipereka kutumikira oyera. Choncho ndikukulimbikitsani kuti,