1 Akorinto 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni. Akula ndi Purisika komanso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa nonsenu, mwa Ambuye. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:19 Nsanja ya Olonda,8/15/2007, tsa. 10
19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni. Akula ndi Purisika komanso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa nonsenu, mwa Ambuye.