2 Akorinto 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikakumana ndi mayesero,* inuyo mumatonthozedwa ndiponso kupulumutsidwa. Tikatonthozedwa, nanunso mumatonthozedwa ndipo zimenezi zimathandiza kuti mupirire mavuto amene nafenso tikukumana nawo. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,11/1/1996, tsa. 14
6 Tikakumana ndi mayesero,* inuyo mumatonthozedwa ndiponso kupulumutsidwa. Tikatonthozedwa, nanunso mumatonthozedwa ndipo zimenezi zimathandiza kuti mupirire mavuto amene nafenso tikukumana nawo.