2 Akorinto 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chiyembekezo chathu pa inu sichikugwedezeka, chifukwa tikudziwa kuti popeza mukukumana ndi mavuto ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, nanunso mudzatonthozedwa.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,11/1/1996, ptsa. 12-13, 14-16
7 Chiyembekezo chathu pa inu sichikugwedezeka, chifukwa tikudziwa kuti popeza mukukumana ndi mavuto ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, nanunso mudzatonthozedwa.+