2 Akorinto 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Abale, tikufuna muzidziwa za mavuto amene tinakumana nawo mʼchigawo cha Asia.+ Tinakumana ndi mavuto aakulu oposa mphamvu zathu, moti tinalibe chiyembekezo choti tikhala ndi moyo.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 163 Nsanja ya Olonda,6/15/2014, tsa. 2312/15/1996, tsa. 2411/1/1996, ptsa. 16-17
8 Abale, tikufuna muzidziwa za mavuto amene tinakumana nawo mʼchigawo cha Asia.+ Tinakumana ndi mavuto aakulu oposa mphamvu zathu, moti tinalibe chiyembekezo choti tikhala ndi moyo.+
1:8 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 163 Nsanja ya Olonda,6/15/2014, tsa. 2312/15/1996, tsa. 2411/1/1996, ptsa. 16-17