2 Akorinto 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipotu tinkangomva ngati taweruzidwa kuti tiphedwe. Izi zinali choncho kuti tisamadzidalire koma tizidalira Mulungu+ amene amaukitsa akufa. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,11/1/1996, ptsa. 16-17
9 Ndipotu tinkangomva ngati taweruzidwa kuti tiphedwe. Izi zinali choncho kuti tisamadzidalire koma tizidalira Mulungu+ amene amaukitsa akufa.