-
2 Akorinto 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ifeyo tili ndi chifukwa chodzitamandira, ndipo chikumbumtima chathu chikutichitiranso umboni, kuti mʼdzikoli, makamaka pakati pa inuyo, tachita zinthu zoyera ndiponso mogwirizana ndi kuona mtima kochokera kwa Mulungu. Tachita zimenezi osati modalira nzeru za mʼdzikoli,+ koma modalira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.
-