-
2 Akorinto 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mukudziwa kale kuti ifeyo ndife chifukwa choti inuyo mudzitamandire, ngati mmene inuyonso mudzakhalire chifukwa choti ifeyo tidzadzitamandire pa tsiku la Ambuye wathu Yesu.
-