-
2 Akorinto 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pamene ndinali ndi cholinga chimenechi, kodi nkhaniyi ndinkaiona mopepuka? Kapena kodi ndinali ndi zolinga zadyera kuti ndikati “Inde, inde” nthawi yomweyo ndisinthe ndinene kuti “Ayi, ayi”?
-