2 Akorinto 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ambiri bwanji, akhala “inde” kudzera mwa iye.+ Choncho kudzeranso mwa iye, “Ame” amanenedwa kwa Mulungu+ ndipo Mulungu amalandira ulemerero kudzera mwa ife. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:20 Nsanja ya Olonda,3/15/2014, tsa. 3112/15/2008, tsa. 13
20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ambiri bwanji, akhala “inde” kudzera mwa iye.+ Choncho kudzeranso mwa iye, “Ame” amanenedwa kwa Mulungu+ ndipo Mulungu amalandira ulemerero kudzera mwa ife.