-
2 Akorinto 1:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mulungu ndi mboni yanga kuti chifukwa chimene sindinabwerere ku Korintoko mpaka pano nʼchakuti sindinafune kudzawonjezera chisoni chanu.
-