-
2 Akorinto 2:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mukakhululukira munthu chilichonse, inenso ndimukhululukira. Ndipo chilichonse chimene ineyo ndakhululukira munthu (ngati chilipo chimene ndakhululuka) ndachita zimenezo chifukwa cha inuyo, pamaso pa Khristu,
-