-
2 Akorinto 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma tikuthokoza Mulungu amene nthawi zonse amatitsogolera limodzi ndi Khristu ngati kuti tikuguba pa chionetsero chonyadira kupambana. Ndipo kudzera mwa ife kafungo konunkhira bwino kodziwa Mulungu kakufalikira paliponse.
-