17 Ifeyo ndife oyenerera. Chifukwa mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri amachitira, koma timalalikira moona mtima mogwirizana ndi zimene ophunzira a Khristu ayenera kuchita. Tatumidwa ndi Mulungu ndipo timachita zimenezi pamaso pa Mulunguyo.