-
2 Akorinto 3:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kodi tikuyambanso kudzichitira umboni tokha? Kapena kodi nʼkofunika kuti ifenso, mofanana ndi anthu ena, tikhale ndi makalata otichitira umboni obwera kwa inu kapena ochokera kwa inu?
-