2 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo atumiki a Mulungu.+ Kalatayo si yolembedwa ndi inki koma ndi mzimu wa Mulungu wamoyo. Si yolembedwa pazolembapo zamiyala+ koma mʼmitima.*+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, ptsa. 13-146/15/1988, tsa. 30
3 Chifukwa zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo atumiki a Mulungu.+ Kalatayo si yolembedwa ndi inki koma ndi mzimu wa Mulungu wamoyo. Si yolembedwa pazolembapo zamiyala+ koma mʼmitima.*+