2 Akorinto 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nawonso malamulo olembedwa amene anapatsidwa ulemerero, achotsedwa ulemererowo chifukwa ulemerero umene wabwera pambuyo pake ndi waukulu kuposa woyambawo.+
10 Nawonso malamulo olembedwa amene anapatsidwa ulemerero, achotsedwa ulemererowo chifukwa ulemerero umene wabwera pambuyo pake ndi waukulu kuposa woyambawo.+