2 Akorinto 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipotu mpaka pano, zimene Mose analemba zikamawerengedwa,+ mitima yawo imakhalabe yophimba.+