2 Akorinto 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwatu ngakhale kuti mavuto* amene tikukumana nawo ndi akanthawi ndiponso aangʼono, akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso womwe ndi wamuyaya,+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:17 Nsanja ya Olonda,2/15/1996, ptsa. 27-28
17 Chifukwatu ngakhale kuti mavuto* amene tikukumana nawo ndi akanthawi ndiponso aangʼono, akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso womwe ndi wamuyaya,+