2 Akorinto 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:10 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, ptsa. 15-16
10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+