-
2 Akorinto 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho popeza timaopa Ambuye, tikupitiriza kukopa anthu ndipo Mulungu akudziwa bwino zolinga zathu. Koma ndikukhulupirira kuti inunso, chikumbumtima chanu chikudziwa bwino zolinga zathu.
-