2 Akorinto 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu ankagwirizanitsa dziko ndi iyeyo kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo zolakwa zawo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolalikira uthenga wothandiza anthu kugwirizananso ndi Mulungu.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:19 Nsanja ya Olonda,12/15/2010, ptsa. 12-1312/15/1998, ptsa. 17-18
19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu ankagwirizanitsa dziko ndi iyeyo kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo zolakwa zawo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolalikira uthenga wothandiza anthu kugwirizananso ndi Mulungu.+