2 Akorinto 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimalankhula nanu momasuka kwambiri komanso ndimakunyadirani kwabasi. Ndalimbikitsidwa kwambiri ndipo ndikusangalala kwambiri pa mavuto onse amene tikukumana nawo.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 15
4 Ndimalankhula nanu momasuka kwambiri komanso ndimakunyadirani kwabasi. Ndalimbikitsidwa kwambiri ndipo ndikusangalala kwambiri pa mavuto onse amene tikukumana nawo.+