-
2 Akorinto 7:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 panopa ndikusangalala. Sikuti ndikusangalala chifukwa munamva chisoni, koma chifukwa chakuti chisonicho chinakuchititsani kulapa. Popeza munamva chisoni mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, zimene tinalemba sizinakuvulazeni.
-