2 Akorinto 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale kuti ndinakulemberani, sindinachite zimenezo chifukwa cha wolakwayo+ kapena wolakwiridwayo ayi, koma kuti zidziwike pamaso pa Mulungu kuti mukufunitsitsa kumvera mawu athu.
12 Ngakhale kuti ndinakulemberani, sindinachite zimenezo chifukwa cha wolakwayo+ kapena wolakwiridwayo ayi, koma kuti zidziwike pamaso pa Mulungu kuti mukufunitsitsa kumvera mawu athu.