-
2 Akorinto 7:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nʼchifukwa chake talimbikitsidwa.
Komabe kuwonjezera pa kulimbikitsidwa, tinasangalalanso kwambiri titaona kuti Tito akusangalala, chifukwa nonsenu munamulimbikitsa.
-