-
2 Akorinto 7:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndinalankhula mokunyadirani kwa iyeyo ndipo simunandichititse manyazi. Koma zimene tinalankhula monyadira kwa Tito nʼzoona, ngati mmene zilili zinthu zonse zimene tinakuuzani.
-