-
2 Akorinto 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipo sanachite zimene tinkayembekezera zokha, koma choyamba anayesetsa ndi mtima wonse kutumikira Ambuye ndipo anatithandiza ifeyo mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu.
-