2 Akorinto 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipereke maganizo anga pamenepa.+ Mungachite bwino kumalizitsa ntchito ya zoperekayi, chifukwa munaiyamba chaka chatha ndiponso munasonyeza mtima wofunitsitsa kuchita zimenezi.
10 Ndipereke maganizo anga pamenepa.+ Mungachite bwino kumalizitsa ntchito ya zoperekayi, chifukwa munaiyamba chaka chatha ndiponso munasonyeza mtima wofunitsitsa kuchita zimenezi.