-
2 Akorinto 8:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsopano malizitsani ntchito imene munaiyamba. Popeza munkafunitsitsa kuchita zimenezi, mumalizitsenso kuzichita mogwirizana ndi zimene muli nazo.
-