-
2 Akorinto 8:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Komanso tikumutumiza pamodzi ndi mʼbale wina amene akutamandidwa mʼmipingo yonse chifukwa cha zimene akuchita zokhudza uthenga wabwino.
-