-
2 Akorinto 9:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tsopano amene amapereka mowolowa manja mbewu kwa wodzala komanso chakudya kuti anthu adye, adzakupatsani mowolowa manja mbewu zoti mudzale. Adzawonjezeranso zokolola za chilungamo chanu.)
-