-
2 Akorinto 9:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mulungu akukudalitsani pa chilichonse kuti muthe kupereka mowolowa manja mʼnjira zosiyanasiyana ndipo anthu akuyamika Mulunguyo chifukwa cha mphatso yanu imene ife tikupereka kwa anthu ena.
-