2 Akorinto 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa utumiki wothandiza anthuwu sikuti ukungothandiza kuti oyerawo apeze zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso kuti anthu ambiri aziyamikira Mulungu mʼmapemphero awo. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 210-213 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, ptsa. 11-12
12 Chifukwa utumiki wothandiza anthuwu sikuti ukungothandiza kuti oyerawo apeze zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso kuti anthu ambiri aziyamikira Mulungu mʼmapemphero awo.