2 Akorinto 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikanakonda kuti ndikadzabwera kumeneko ndisadzachite zinthu zazikulu zimene ndikuyembekezera kudzachita potsutsana ndi anthu ena amene akuona kuti ifeyo tinachita zinthu ngati anthu amʼdzikoli.*
2 Ndikanakonda kuti ndikadzabwera kumeneko ndisadzachite zinthu zazikulu zimene ndikuyembekezera kudzachita potsutsana ndi anthu ena amene akuona kuti ifeyo tinachita zinthu ngati anthu amʼdzikoli.*