-
2 Akorinto 10:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mukuona zinthu potengera maonekedwe akunja. Ngati aliyense amakhulupirira mumtima mwake kuti ndi wotsatira Khristu, aganizirenso kuti: Mmene zilili kuti iyeyo amatsatira Khristu, ifenso timatsatira Khristu.
-