2 Akorinto 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sitidziona ngati ndife ofanana ndi anthu amene amadzikweza komanso sitidziyerekezera ndi anthuwo.+ Koma anthu amenewo akamayezana okhaokha pogwiritsa ntchito mfundo zawo nʼkumadziyerekezera okhaokha, samvetsa chilichonse.+
12 Sitidziona ngati ndife ofanana ndi anthu amene amadzikweza komanso sitidziyerekezera ndi anthuwo.+ Koma anthu amenewo akamayezana okhaokha pogwiritsa ntchito mfundo zawo nʼkumadziyerekezera okhaokha, samvetsa chilichonse.+