2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mofanana ndi mmene njoka inanamizira Hava ndi chinyengo chake,+ nkhawa yanga ndi yakuti mwina maganizo anunso angapotozedwe moti simungakhalenso oona mtima ndiponso oyera. Koma munthu wa Khristu amafunika kukhala woona mtima komanso woyera.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:3 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 192 Nsanja ya Olonda,10/15/2002, tsa. 82/15/1987, ptsa. 11-12
3 Mofanana ndi mmene njoka inanamizira Hava ndi chinyengo chake,+ nkhawa yanga ndi yakuti mwina maganizo anunso angapotozedwe moti simungakhalenso oona mtima ndiponso oyera. Koma munthu wa Khristu amafunika kukhala woona mtima komanso woyera.+
11:3 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 192 Nsanja ya Olonda,10/15/2002, tsa. 82/15/1987, ptsa. 11-12