2 Akorinto 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kapena kodi ndinalakwa pamene ndinadzichepetsa kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalalikira mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kulipira?+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:7 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 148-150 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2019, tsa. 4
7 Kapena kodi ndinalakwa pamene ndinadzichepetsa kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalalikira mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kulipira?+