2 Akorinto 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndikulankhula choonadi cha Khristu, choncho sindidzasiya kudzitamandira+ mʼmadera a ku Akaya.