2 Akorinto 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipitiriza kuchita zimene ndikuchita,+ kuti nditsekereze anthu amene akuyesetsa kupeza chifukwa chonenera kuti ndi ofanana ndi ife pa zinthu zimene amadzitamandira.
12 Ndipitiriza kuchita zimene ndikuchita,+ kuti nditsekereze anthu amene akuyesetsa kupeza chifukwa chonenera kuti ndi ofanana ndi ife pa zinthu zimene amadzitamandira.