-
2 Akorinto 11:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndikubwerezanso kunena kuti, munthu aliyense asandione ngati wopanda nzeru. Koma ngati mukundiona kuti ndine wopanda nzeru, ingovomerezani kuti ndi mmene ndilili, kuti nanenso ndidzitame pangʼono.
-