-
2 Akorinto 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Zimene ndikulankhulazi, sindikulankhula ngati munthu wotsatira chitsanzo cha Ambuye. Koma ngati munthu wopanda nzeru ndiponso wodzitama ndi wodzidalira kwambiri.
-