-
2 Akorinto 11:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndipotu mumalolera aliyense wokuchititsani kukhala akapolo, wotenga zinthu zanu, wolanda zimene muli nazo, wodziona kuti ndi wapamwamba kuposa inuyo ndiponso aliyense wokuwombani mbama.
-